Saturday, June 23, 2007

Letter in Chichewa

Wawa!
Dzina langa ndine Kyla Firby, ndi ndinachokela ku Canada. Ndili ndi zaka 23, ndi ndine ophunzira. Ndidabwera ku Malawi mwezi wathawu. Ndilikuphunzila kuyankhula ndi kulemba Chichewa. Ndimagwira ntchito ku EWB Canada, ndi BERDO ku Malawi. Ndi makhala ku Bwanje kwa Mr. ndi Mrs. Shara. Ndi maphunzila kuphika nsima, kusesa nymuba, kuchapa chovala, ndi kudzuka m’mamawa. Ndimadya chimanga, mtedza, kabichi, nthochi, mbatata, maungu, lepu, mbuzi, mazira, nkhuku, ndi nsomba. Ndidapita ku Blantyre sabata latha. Ndidzapita ku Lilongwe sabata lamawa. Ndikufuna kuona EWB mnzanga ku Lilongwe. Ndidzapita ndi abwenzi ku Peace Corps. Akukhala ku Sharpavale.

Ndilikusowa inunonse.
Ndidzawaona mu Ogasiti.

Kyla Firby

Khalani omasuk!

Translation:

Hey!
My name is Kyla Firby, and I come from Canada. I am 23 years old and I am a student. I came to Malawi last month. I am learning to speak and write Chichewa. I work for EWB Canada and BERDO in Malawi. I live with Mr. and Mrs. Shara. I have learned to cook nsima, sweep the house, wash my clothes, and get up early in the morning. I eat maize, groundnuts (peanuts), cabbage, bananas, sweet potatoes, pumpkin, rape, goat, eggs, chicken, and fish. I went to Blantyre last week. I will go to Lilongwe next week. I want to see my EWB friends in Lilongwe. I am going to go with my friend from Peace Corps. He is living in Sharpavale.

I miss you all.
I will see you in August.

Kyla Firby

Be Free!

2 comments:

Tom said...

Moni, Kyla
Dzina langa ndine Tom O’Dwyer, Sr. Ndakondwa ndilikuphunzila kuyankhula muli kulemba Chichewa.

Ndiri kudya chakudya muli mayi mudzi Windsor, dziko Canada. Ndili wosangalala. Heidi kuseka SMART galimoto. Muli mayi chiphadzuwa—ngenge.

Zikomo,

Tom (the older one)

Tom said...

Moni, Kyla
Dzina langa ndine Tom O’Dwyer, Sr. Ndakondwa ndilikuphunzila kuyankhula muli kulemba Chichewa.

Ndiri kudya chakudya muli mayi mudzi Windsor, dziko Canada. Ndili wosangalala. Heidi kuseka SMART galimoto. Muli mayi chiphadzuwa—ngenge.

Zikomo,

Tom (the older one)

Team Malawi 2007

Team Malawi 2007
The Malawi team meets for the first time in Calgary during the EWB National Conference